Ndiwe wanga, beby yanga, nkazi wanga Baby ine ndimakonda iwe wekha Baby ine ndimafuna iwe wekha Love yanga ndimapatsa iwe wekha Iwe ndiwe wanga wanga Future Mother wa ana anga Madamo a nyumba yanga
Iwe ndiwe wanga wanga Future Mother wa ana anga Madamo a nyumba yanga Ndiwe wekha unatenga
Padziko assanje alipo ambiri Tiye tikondane m'mene tililj Iwe ndi ine tipangue mbiri, (huu mbiri) Opanda iwe sinditha kukhala Opanda iwe baby ine ndimamala Zokamba kamba ossawavela Kukhala ndiwe, baby ine ndimamala